Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 10/15 tsamba 3
  • Kodi Mungatani Kuti Mawu a Mulungu Azikuthandizani pa Moyo Wanu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungatani Kuti Mawu a Mulungu Azikuthandizani pa Moyo Wanu?
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Nkhani Yofanana
  • Kupindula ndi Kuŵerenga Baibulo Tsiku ndi Tsiku
    Nsanja ya Olonda—1995
  • Chitani Khama pa Kuŵerenga
    Pindulani ndi Sukulu ya Utumiki wa Mulungu
  • Zimene Mungachite Kuti Muzipindula Powerenga Baibulo
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kuŵerenga Baibulo—N’kopindulitsa ndi Kosangalatsa
    Nsanja ya Olonda—2000
Onani Zambiri
Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
km 10/15 tsamba 3

Kodi Mungatani Kuti Mawu a Mulungu Azikuthandizani pa Moyo Wanu?

Kuwerenga Baibulo tsiku lililonse, kungatithandize kuti tikhale “ozikika mozama” komanso ‘okhazikika m’chikhulupiriro.’ (Akol. 2:6, 7) Koma kuti Mawu a Mulungu azititsogolera, tiyenera kuganizira kwambiri zimene tawerengazo komanso kuyesetsa kuzitsatira pa moyo wathu. (Aheb. 4:12; Yak. 1:22-25) Lemba la Yoswa 1:8 limatiuza zinthu zitatu zimene tiyenera kuchita. (1) Tiziwerenga Mawu Mulungu “usana ndi usiku.” (2) ‘Tizisinkhasinkha’ zomwe tawerengazo. Kuti zimenezi zitheke, tisamawerenge mothamanga koma tiziwerenga modekha kuti tizitha kuganizira zimene tikuwerengazo komanso mmene zinthu zinaliri pamene mawuwo ankalembedwa. (3) Tiziyesetsa ‘kutsatira zonse zolembedwamo.’ Tikamachita zinthu zitatu zimenezi, tidzakhala “ndi moyo wopambana” komanso tidzachita “zinthu mwanzeru.”

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena