Imbirani Yehova Mosangalala NAMBALAMUTUMLOZERA YEHOVA 1-12 NYIMBO 1 Makhalidwe a Yehova NYIMBO 2 ‘Dzina Lanu Ndi Yehova’ NYIMBO 3 Ndinu Mphamvu Ndi Chiyembekezo Chathu Ndipo Timakudalirani NYIMBO 4 “Yehova Ndi M’busa Wanga” NYIMBO 5 Ntchito Zodabwitsa za Mulungu NYIMBO 6 Kumwamba Kumalengeza Ulemerero wa Mulungu NYIMBO 7 Yehova Ndi Mphamvu Yathu NYIMBO 8 Yehova Ndi Pothawirapo Pathu NYIMBO 9 Yehova Ndi Mfumu NYIMBO 10 Tamandani Yehova Mulungu Wathu NYIMBO 11 Chilengedwe Chimatamanda Mulungu NYIMBO 12 Yehova Mulungu Wamkulu YESU/DIPO 13-20 NYIMBO 13 Titsanzire Yesu NYIMBO 14 Tamandani Mfumu Yatsopano Yolamulira Dziko Lapansi NYIMBO 15 Tamandani Mwana Woyamba Kubadwa wa Yehova NYIMBO 16 Tamandani Yehova Chifukwa cha Mwana Wake Wodzozedwa NYIMBO 17 “Ndikufuna” NYIMBO 18 Tikuthokoza Chifukwa cha Dipo NYIMBO 19 Chakudya Chamadzulo cha Ambuye NYIMBO 20 Munapereka Mwana Wanu Wobadwa Yekha UFUMU 21-24 NYIMBO 21 Muziika Ufumu Pamalo Oyamba NYIMBO 22 Ufumu Umene Ukulamulira Kumwamba Ubwere NYIMBO 23 Yehova Wayamba Kulamulira NYIMBO 24 Bwerani Kuphiri la Yehova ODZOZEDWA NDI ANKHOSA ZINA 25-27 NYIMBO 25 Chuma Chapadera NYIMBO 26 “Munachitiranso Ine” NYIMBO 27 Ulemerero wa Ana a Mulungu Udzaonekera UBWENZI NDI YEHOVA 28-40 NYIMBO 28 Tikhale pa Ubwenzi Ndi Yehova NYIMBO 29 Tizichita Zinthu Zogwirizana Ndi Dzina Lathu NYIMBO 30 Atate Wanga, Mulungu Wanga Ndiponso Bwenzi Langa NYIMBO 31 Muziyenda Ndi Mulungu NYIMBO 32 Khalani Kumbali ya Yehova NYIMBO 33 Umutulire Yehova Nkhawa Zako NYIMBO 34 Kuchita Zinthu Mokhulupirika NYIMBO 35 “Muzitha Kusankha Zinthu Zimene Ndi Zofunikadi Kwambiri” NYIMBO 36 Titeteze Mtima Wathu NYIMBO 37 Kutumikira Yehova Ndi Moyo Wonse NYIMBO 38 Adzakulimbitsa NYIMBO 39 Tipange Mbiri Yabwino kwa Mulungu NYIMBO 40 Kodi Ndife A Ndani PEMPHERO 41-47 NYIMBO 41 Imvani Pemphero Langa NYIMBO 42 Pemphero la Mtumiki wa Mulungu NYIMBO 43 Pemphero Lothokoza NYIMBO 44 Pemphero la Munthu Wovutika NYIMBO 45 “Zimene Ndimaganizira Mozama” NYIMBO 46 Tikukuthokozani Yehova NYIMBO 47 Muzipemphera kwa Yehova Nthawi Zonse KUDZIPEREKA 48-52 NYIMBO 48 Tiziyenda ndi Yehova Tsiku Lililonse NYIMBO 49 Tizisangalatsa Mtima wa Yehova NYIMBO 50 Pemphero Langa Losonyeza Kudzipereka NYIMBO 51 Tadzipereka kwa Mulungu NYIMBO 52 Kudzipereka Monga Mkhristu UTUMIKI WATHU 53-84 NYIMBO 53 Kukonzekera Kupita Kokalalikira NYIMBO 54 “Njira Ndi Iyi” NYIMBO 55 Musawaope NYIMBO 56 Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha NYIMBO 57 Tizilalikira Anthu a Mitundu Yonse NYIMBO 58 Kufufuza Anthu Okonda Mtendere NYIMBO 59 Tamandani Ya NYIMBO 60 Akamvera Adzapeza Moyo NYIMBO 61 Pitani Patsogolo Mboninu NYIMBO 62 Nyimbo Yatsopano NYIMBO 63 Ndife Mboni za Yehova NYIMBO 64 Tizigwira Ntchito Yokolola Mosangalala NYIMBO 65 Pita Patsogolo NYIMBO 66 Lengezani Uthenga Wabwino NYIMBO 67 “Lalikira Mawu” NYIMBO 68 Tizifesa Mbewu za Ufumu NYIMBO 69 Pitirizani Kulalikira za Ufumu NYIMBO 70 Fufuzani Anthu Oyenerera NYIMBO 71 Ndife Gulu Lankhondo la Yehova NYIMBO 72 Tikulalikira Choonadi Chonena za Ufumu NYIMBO 73 Tithandizeni Kukhala Olimba Mtima NYIMBO 74 Tiimbile Limodzi Nyimbo ya Ufumu NYIMBO 75 “Ine Ndilipo! Nditumizeni” NYIMBO 76 Kodi Mumamva Bwanji? NYIMBO 77 Kuwala M’dziko Lamdima NYIMBO 78 Kuphunzitsa Mawu a Mulungu NYIMBO 79 Athandizeni Kukhala Olimba NYIMBO 80 “Talawani Ndipo Muona Kuti Yehova Ndi Wabwino” NYIMBO 81 Moyo wa Mpainiya NYIMBO 82 “Muzionetsa Kuwala Kwanu” NYIMBO 83 “Kunyumba ndi Nyumba” NYIMBO 84 Tizilalikira Modzipereka KUSONKHANA PAMODZI 85-93 NYIMBO 85 Tizilandilana NYIMBO 86 Tiziphunzitsidwa NYIMBO 87 Bwerani Mudzalimbikitsidwe NYIMBO 88 Ndiphunzitseni Njira Zanu NYIMBO 89 Mvera Kuti Udalitsidwe NYIMBO 90 Tizilimbikitsana NYIMBO 91 Ntchito Yomwe Tagwira Chifukwa cha Chikondi NYIMBO 92 Malo Odziwika Ndi Dzina Lanu NYIMBO 93 Mudalitse Msonkhano Wathu MALEMBA 94-98 NYIMBO 94 Tikuthokoza Mulungu Potipatsa Mawu Ake NYIMBO 95 Kuwala Kukuwonjezerekabe NYIMBO 96 Baibulo Ndi Chuma NYIMBO 97 Mawu a Mulungu Amatithandiza Kukhala Ndi Moyo NYIMBO 98 Malemba Anauziridwa Ndi Mulungu UBALE WATHU 99-103 NYIMBO 99 Abale Ambirimbiri NYIMBO 100 Alandireni Bwino NYIMBO 101 Tizichita Zinthu Mogwirizana NYIMBO 102 “Muzithandiza Ofooka” NYIMBO 103 Abusa Ndi Mphatso MAKHALIDWE A MULUNGU 104-130 NYIMBO 104 Mzimu Woyera Ndi Mphatso Yochokera kwa Mulungu NYIMBO 105 “Mulungu Ndi Chikondi” NYIMBO 106 Tikulitse Khalidwe la Chikondi NYIMBO 107 Tizitsanzira Chikondi cha Mulungu NYIMBO 108 Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu NYIMBO 109 Tizikondana Kwambiri Kuchokera Mumtima NYIMBO 110 “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka” NYIMBO 111 Tili Ndi Zifukwa Zambiri Zokhalira Osangalala NYIMBO 112 Yehova Ndi Mulungu Wamtendere NYIMBO 113 Yehova Amatipatsa Mtendere NYIMBO 114 “Khalani Oleza Mtima” NYIMBO 115 Tizithokoza Kuleza Mtima kwa Mulungu NYIMBO 116 Kukoma Mtima Ndi Kofunika Kwambiri NYIMBO 117 Khalidwe la Ubwino NYIMBO 118 “Tiwonjezereni Chikhulupiriro” NYIMBO 119 Tikhale Ndi Chikhulupiriro Cholimba NYIMBO 120 Tikhale Ofatsa Ngati Khristu NYIMBO 121 Timafunika Kukhala Odziletsa NYIMBO 122 Khalani Olimba Komanso Osasunthika NYIMBO 123 Tizigonjera Mulungu Mokhulupirika NYIMBO 124 Tizikhulupirika Nthawi Zonse NYIMBO 125 “Osangalala Ndi Anthu Achifundo” NYIMBO 126 Khala Maso, Khala Wolimba, Khala Wamphamvu NYIMBO 127 Mtundu wa Munthu Amene Ndiyenera Kukhala NYIMBO 128 Tipirire Mpaka Mapeto NYIMBO 129 Tipitirizebe Kupirira NYIMBO 130 Muzikhululuka BANJA/MABWENZI 131-138 NYIMBO 131 “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi” NYIMBO 132 Tsopano Ndife Thupi Limodzi NYIMBO 133 Lambirani Yehova Mudakali Achinyamata NYIMBO 134 Ana Ndi Mphatso Yochokera kwa Mulungu NYIMBO 135 Yehova Akutipempha Kuti: “Mwana Wanga Khala Wanzeru” NYIMBO 136 Yehova “Akulipire Mokwanira” NYIMBO 137 Akazi Achikhristu Okhulupirika NYIMBO 138 Imvi Ndi Chisoti cha Ulemerero CHIYEMBEKEZO CHATHU 139-147 NYIMBO 139 Yerekezerani Kuti Muli M’dziko Latsopano NYIMBO 140 Tidzakhala Ndi Moyo Wosatha NYIMBO 141 Moyo Ndi Wodabwitsa NYIMBO 142 Tigwire Mwamphamvu Chiyembekezo Chathu NYIMBO 143 Pitirizani Kugwira Ntchito, Kukhala Maso ndi Kudikira NYIMBO 144 Mukhulupirikebe NYIMBO 145 Mulungu Watilonjeza Paradaiso NYIMBO 146 “Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga Ndi Zatsopano” NYIMBO 147 Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha KUPULUMUTSIDWA/KUUKITSIDWA 148-151 NYIMBO 148 Yehova Amapereka Populumukira NYIMBO 149 Tiimbire Yehova Chifukwa Wapambana NYIMBO 150 Bwerani kwa Mulungu Kuti Mupulumuke NYIMBO 151 Iye Adzaitana NYIMBO ZATHU 152-161 NYIMBO 152 Malo Amene Adzachititsa Kuti Mulemekezedwe NYIMBO 153 Ndithandizeni Ndikhale Wolimba Mtima NYIMBO 154 Chikondi Sichitha NYIMBO 155 Chimwemwe Chosatha NYIMBO 156 Ndi Maso a Chikhulupiriro NYIMBO 157 Kudzakhala Mtendere NYIMBO 158 “Sadzachedwa” NYIMBO 159 M’patseni Yehova Ulemerero NYIMBO 160 “Uthenga Wabwino” NYIMBO 161 “Ndimasangalala Kuchita Zimene Mumafuna”