Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsamba 1
  • Zitsanzo za Ulaliki

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zitsanzo za Ulaliki
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • GALAMUKANI!
  • KUPHUNZITSA CHOONADI
  • KODI BAIBULO LILI NDI UTHENGA WOTANI? (bm)
  • LEMBANI ULALIKI WANUWANU
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Zitsanzo za Ulaliki
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 February tsamba 1
Mtsikana wa Mboni akufotokozera anzake a m’kalasi zimene walemba

Mtsikana wa Mboni akufotokozera anzake a m’kalasi zimene walemba zokhudza chilengedwe

Zitsanzo za Ulaliki

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 1 2017 | N’chifukwa Chiyani Achinyamata Ambiri Akudwala Matenda Ovutika Maganizo?

Funso: Zikuoneka kuti achinyamata ambiri masiku ano akudwala matenda ovutika maganizo. Kodi mukuganiza kuti n’chiyani chingathandize kuchepetsa vutoli?

Perekani Magaziniyo: Magazini iyi ikufotokoza mfundo zimene zingathandize achinyamata amene akudwala matendawa ndiponso mmene makolo awo angawathandizire.

KUPHUNZITSA CHOONADI

Baibulo lotsegula

Funso: Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tikhale ndi banja losangalala?

Lemba: Aef. 5:33

Zoona Zake: Banja limayenda bwino mwamuna ndi mkazi akamakondana ndiponso kulemekezana.

KODI BAIBULO LILI NDI UTHENGA WOTANI? (bm)

Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?

Funso: Anthu ambiri amene talankhula nawo amadandaula chifukwa cha zinthu zoipa zimene zikuchitika m’dzikoli. Kodi mukuganiza kuti Mulungu adzathetsa mavutowa?

Lemba: Sal. 37:11

Perekani Kabukuko: Baibulo limanena kuti posachedwapa Mulungu athetsa mavuto. Limafotokozanso mfundo zimene zingatithandize kulimbana ndi mavuto athu panopa. Kabuku aka kakufotokoza zambiri pa nkhaniyi.

LEMBANI ULALIKI WANUWANU

Potengera zitsanzozi, konzani njira imene mungagwiritse ntchito.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena