February Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya February 2017 Zitsanzo za Ulaliki February 6-12 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 47-51 Kumvera Yehova Kumabweretsa Madalitso February 13-19 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 52-57 Khristu Anavutika Chifukwa cha Ife MOYO WATHU WACHIKHRISTU Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikhulupirira Kwambiri Mlengi February 20-26 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 58-62 ‘Tikalengeze za Chaka cha Yehova Chokomera Anthu Mtima’ MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizigwiritsa Ntchito Mwanzeru Mabuku Ndiponso Magazini February 27–March 5 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 63-66 Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu