Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsamba 6
  • February 27–March 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 27–March 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 February tsamba 6

February 27–March 5

YESAYA 63-66

  • Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano”: (10 min.)

    • Yes. 65:17​—“Zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso” (ip-2 382 ¶23)

    • Yes. 65:18, 19​—Tidzasangalala kwambiri (ip-2 384 ¶25)

    • Yes. 65:21-23​—Tizidzagwira ntchito zosangalatsa ndipo sitidzakhalanso ndi nkhawa (w12 9/15 9 ¶4-5)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 63:5​—Kodi ukali wa Mulungu umamuchirikiza bwanji? (w07 1/15 11 ¶7)

    • Yes. 64:8​—Kodi Yehova amagwiritsa ntchito bwanji udindo wake monga Wotiumba? (w13 6/15 25 ¶3-5)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 63:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Aef. 5:33​—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) 1 Tim. 5:8; Tito 2:4, 5​—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) Yes. 66:23; w06 11/1 30-31 ¶14-17​—Mutu: Misonkhano Ndi Yofunika Kwambiri pa Kulambira Kwathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 129

  • “Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu” (Yes. 65:17, 18; Aroma 12:12): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 18 ¶14-21 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 161

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena