Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsamba 7
  • Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • “Zinthu Zakale Sizidzakumbukiridwanso”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • “Taonani! Zinthu Zonse Zimene Ndikupanga N’zatsopano”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Dziko Latsopano Limene Mulungu Walonjeza
    Dikirani!
  • Mmene “Miyamba Yatsopano ndi Dziko Lapansi Latsopano” Zikuyambira
    Kupulumuka Kuloŵa m’Dziko Lapansi Latsopano
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 February tsamba 7
Yesu akulamulira monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 63-66

Tidzasangalala Kwambiri ndi Kumwamba Kwatsopano Komanso Dziko Lapansi Latsopano

Zimene Mulungu analonjeza mu chaputala 65 cha Yesaya zidzachitikadi ndipo n’chifukwa chake Yehova anazinena ngati zachitika kale

Yehova akulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso

65:17

Kodi kumwamba kwatsopano n’chiyani?

  • Boma latsopano limene lidzathetse zinthu zopanda chilungamo padzikoli

  • Linakhazikitsidwa mu 1914 pamene Khristu anaikidwa kukhala Mfumu ya Ufumu wa Mulungu

Kodi dziko lapansi latsopano n’chiyani?

  • Anthu ochokera m’mayiko, zinenero komanso m’mitundu yosiyanasiyana omwe amamvera ndi mtima wonse boma latsopano la kumwamba

Kodi mawu akuti zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso akutanthauza chiyani?

  • Mulungu adzachotsa mavuto onse amene amachititsa kuti tizikumbukira zinthu zoipa zimene zinatichitikira.

  • Anthu okhulupirika adzasangalala kwambiri ndi moyo ndipo tsiku lililonse azidzachita zinthu zoti akazikumbukira, zizidzawasangalatsa

    Munthu wolumala wayamba kuyenda, mwana akusewera ndi kambuku, banja likuthyola zipatso, munthu wakumana ndi m’bale wake yemwe wangoukitsidwa kumene
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena