Akumanga Nyumba ya Ufumu ku Australia
Zimene Tinganene
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti mfundo zimene zingatithandize tikaferedwa?
Lemba: 2 Akor. 1:3, 4
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?
○●○ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA
Funso: Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?
Lemba: Mlal. 9:5, 10
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi anthu amene anamwalira angadzakhalenso ndi moyo?
○○●ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI
Funso: Kodi anthu amene anamwalira angadzakhalenso ndi moyo?
Lemba: Mac. 24:15
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi anthu amene anamwalira adzaukitsidwira kuti?