MTIMA WODEKHA NDIWO MOYO WA MUNTHU”
Mawu amenewa opezeka pa Miyambo 14:30, analembedwa pafupi-fupi zaka 3,000 zapitazo! Ndipo amaonetsa kuti malangizo a m’Baibo ni othandiza nthawi zonse. Ngati mufuna kuphunzila zambili, yendani pa webusaiti ya jw.org ku Chichewa. Mudzapezapo mavidiyo, zithunzi na mavidiyo a tukadoli, kufunsa anthu mafunso, komanso nkhani zosiyana-siyana zothandiza, zimene ziphatikizapo nkhani zimene zingakuthandizeni kucepetsa nkhawa. Zina mwa nkhani zimene mudzapeza ni izi: