Mlozela Nkhani
Cidziŵitso: Pa mlozela nkhani ali pansipa, nambala yoyamba ni mutu wa nkhani, yotsatila ni nambala ya ndime. Mwacitsanzo, pansi pa “Zilengezo” nkhani yoyamba imene alozako ni “zopeleka: 12:6.” Izi zitanthauza kuti nkhani yokhudza zopeleka ipezeka pa Mutu 12, ndime 6.
Akalinde: 11:14
Akulu
amaikidwa mwa ndondomeko ya umulungu: 4:8
kukalamila: 5:22
kusunga ciyelo ca mpingo: 14:19-40
mamiting’i: 5:37
mgwilizano pakati pawo: 5:21
mmene tiyenela kuwaonela: 3:14; 5:38-39
okalamba kapena odwalila: 5:23-24
tumagulu na tumagulu toyesela: 9:42-44
ziyenelezo: 5:4-20
Alongo
ngati palibe abale oyenelezedwa: 6:9; 7:23
masukulu a zaumulungu: 10:17-18
utumiki wa mamangidwe: 10:21
Ana
abale acinyamata kukalamila: 6:14
kucita colakwa: 14:37
kupita patsogolo kuuzimu: 8:13-15; 10:26; masa. 179-181
kuthandiza makolo olemala komanso ambuye awo: 12:14
zocitika za kusukulu: 13:22-24
Anthu osauka: 12:12-15
Apainiya apadela: 10:11, 14, 17-18
Apainiya: 10:11-14
Apainiya othandiza: 10:11-12
Atumiki othandiza
kukalamila: 6:14
kuonetsa kuyamikila: 6:1-2, 15
ziyenelezo: 6:3-6
Bungwe Lolamulila
kulidziŵa: 3:1-6
kuonetsa kuti timalidalila: 3:12-15
zifukwa zake tiyenela kutsatila zitsogozo zake: 3:9-11; 4:9-11
Cicilikizo ca ndalama
ca padziko lonse: 11:15; 12:2-4
dela: 12:8-11
Cikumbutso: 7:28-30
Colakwa
(Onaninso Kudzilekanitsa; Kucotsedwa mu mpingo; Kuika cizindikilo oyenda mosalongosoka; Kusemphana Maganizo; Kubwezeletsedwa)
ana: 14:37
cilengezo cake: 14:24, 29, 33, 39-40
colakwa cacikulu: 14:21-33
kulakwila Mkhristu wina: 14:5-6, 13-20
ofalitsa osabatizika: 14:38-40
Gawo
la kagulu komanso laumwini: 9:31-34
madela a zinenelo zosiyana-siyana: 9:36-37
zofunikila kulemba: 9:31
Gulu
gawo lakumwamba: 1:8-13
JW.ORG: 9:24-25
Kabuku ka Misonkhano ya Umoyo na Utumiki: 7:14-18
“Kapolo wokhulupilika ndi wanzelu”
kumudalila: 3:12-15
kumugonjela: 15:7
kumuzindikila: 3:4-6
Khadi ya Mpingo Yolembapo Nchito za Wofalitsa: 5:44; 8:10, 30
Komiti ya Utumiki
(Onani Komiti ya Utumiki ya Mpingo)
Komiti ya Utumiki ya Mpingo: 5:35
Kubwezeletsedwa: 14:34-36
Kucotsedwa Mumpingo: 14:25-29
Kudzilekanitsa: 14:30-33
Kudzipatulila na ubatizo
(Onani Ubatizo)
Kugonjela
(Onani Umutu)
Kuika cizindikilo oyenda mosalongosoka: 14:9-12
Kuikidwa kukhala mtumiki wa Mulungu: 8:3
Kukatumikila kosoŵa: 10:6-9
Kukhala acitsanzo cabwino
tanthauzo lake: 6:9
Kulalikila uthenga wabwino
acicepele: 8:13-15
kucitila lipoti: 8:19-29, 31-36
kukumana kotenga malangizo a ulaliki: 7:20-21
kulimbikitsa phunzilo la Baibo kulalikila mwamwayi: 8:5
kunyumba na nyumba: 9:3-9
kuseŵenzetsa jw.org: 9:24-25
kutsogolela: 5:3, 17, 29-33; 6:4
mabuku: 9:22-23
madela a zinenelo zosiyana-siyana: 9:35-44
magawo: 9:30-34
maonekedwe aumwini: 13:12
maulendo obwelelako: 9:14-15
mwamwayi: 9:26-29
ni nchito yocokela kwa Mulungu: 8:2
pa ciletso: 17:13-18
thandizo kwa munthu payekha: 5:28-29, 33; 7:21; 9:7, 15, 19
udindo wa woyang’anila utumiki: 5:28
ulaliki wa kagulu: 9:45-46
ulaliki wapoyela: 9:11-12
zaka za zana loyamba: 8:1-2; 9:1, 4
Kusemphana Maganizo
kuthetsa mavuto akulu-akulu: 14:13-20
kuthetsa mavuto ang’ono-ang’ono: 14:5-6
Mabuku
kusamalila zogwilitsila nchito: 12:16
madela a zinenelo zosiyana-siyana: 9:36, 38
ndalama zoyendetsela nchito yathu: 12:2-4
ni othandiza mu ulaliki: 9:22-23
Mabungwe alamulo: 4:12
Mabwalo a Misonkhano: 11:18-21
Madela a zinenelo zosiyana-siyana: 9:35-44
makalasi ophunzila cinenelo: 10:10
ngati mwininyumba akamba citundu cina: 9:38-41
tumagulu na tumagulu toyesela: 9:42-44
(Ma)komiti
Ya dziko: 5:53
Ya Utumiki ya Mpingo: 5:35
Yolankhulana ndi Acipatala: 5:40
Yosamalila Nyumba ya Ufumu: 11:8
Makomiti aciweluzo: 14:21-28, 34-37
Makomiti Olankhulana ndi Acipatala, na Tumagulu Toyendela Odwala: 5:40
Malilo: 11:10-11
Malipoti
kufunika kwake: 8:19-22, 31-36
mukapita kwina: 8:30
oyang’anila madela: 5:46, 50; 9:44
Maphunzilo a Baibo
kucitila lipoti: 8:26
kulimbikitsa wophunzila kuti azilalikila mwamwayi: 8:5
kutsogolela wophunzila ku gulu: 9:20-21
zofunika: 9:16-17
Mavalidwe na kudzikongoletsa
atumiki othandiza: 6:5
awo amene amapatsidwa mwayi wapadela wotumikila: 6:9
kukaceza ku Beteli: 13:13
mu ulaliki: 13:12
zocitika zosangulutsa: 13:14
Mayeso, mayeselo: 13:4-5; 17:4-19
Mgonelo wa Ambuye: 7:28-30
Mgwilizanitsi wa Bungwe la Akulu
kucezela kwa woyang’anila dela: 5:42-44
kupenda maakaunti: 12:7
Msonkhano wa Umoyo na Utumiki: 7:18
ofunsila ubatizo: 8:18; masa. 208-212
udindo wake: 5:26
Mgwilizano
kusunga mgwilizano: 17:20
madalitso: 4:15; 5:57; 13:30-31
pansi pa umutu wa Yesu: 2:9-11; 4:10-11
wa padziko lonse: 16:6-11
Misonkhano
Aisiraeli: 11:1
akalinde: 11:14
akulu: 5:37
ana kupezekapo: 11:13
colinga: 7:1-2
kufunika kwake: 3:12; 7:4, 27; 15:7
kukambilana zamalonda: 13:27
kutenga malangizo a ulaliki: 7:20-21; 9:45
malo osonkhanila: 11:1-5, 18-19
misonkhano yacigawo: 7:25-26
misonkhano yadela: 7:24
mkati mwa kucezela kwa woyang’anila dela: 5:43, 47
nkhani ya anthu onse: 7:5-10
pamene mlongo atsogoza: 7:23
panthawi ya ciletso: 17:15-17
Phunzilo la Baibo la Mpingo: 7:17
Phunzilo la Nsanja ya Mlonda: 7:11-13
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu: 7:14-19
Zaka za zana loyamba: 7:3; 11:2
Misonkhano Yacigawo: 7:25-27
Misonkhano Yadela
(Onani Msonkhano Wadela)
Mpingo
(Onaninso Nyumba ya Ufumu; Misonkhano)
mwa dongosolo la umulungu: 1:3; 4:4-11
umodzi: 13:28-30
watsopano ndiponso waung’ono: 7:22-23
Msonkhano wadela
kakonzedwe kake: 5:49
malo osonkhanila: 11:18
ndalama zoyendetsela: 12:8-11
Nchito yakuthupi: 13:25-26
Nkhani ya anthu onse: 7:5-10
Nyumba ya Ufumu
kuigwilitsila nchito mwapadela: 11:10-11
kuyeletsa na kusamalila: 11:7-8
kumanga: 10:21-23; 11:4-5, 15-17
kupatulila: 11:4
laibulali: 7:19
mipingo ingapo: 11:8-9
ndalama zogwilitsila nchito: 11:6; 12:5-6
Ofalitsa
(Onani Ofalitsa a mpingo; Ofalitsa Obatizika)
Ofalitsa a mpingo
(Onaninso Ofalitsa osabatizika)
acicepele: 8:13-14
kusamuka: 8:30
olemala: 8:29
thandizo kwa munthu payekha: 5:28-29, 33; 7:21; 9:7, 15, 19
watsopano: 8:5-6
ziyenelezo: 8:8
Ofalitsa osabatizika
ana: 8:13-15
colakwa: 14:38-40
pomanga Nyumba ya Ufumu kapena kuikonzanso: 11:17
ziyenelezo: 8:6-12
Ofesi ya Nthambi
mavalidwe na kudzikongoletsa pokaceza: 13:13
pamene kulumikizana nayo kwaduka: 17:15-17
udindo wake: 4:13
zopeleka ku: 12:2-4
Oimilako Likulu: 5:55-56
Oyang’anila
(Onani Akulu)
Phunzilo la Nsanja ya Mlonda: 7:11-13
Thandizo Pakagwa za Mwadzidzidzi: 12:15; 16:11
Tumagulu twa ulaliki
kugaŵila ku kagulu: 5:35
kukumana kotenga malangizo a ulaliki: 7:20-21
kuyeletsa nyumba ya Ufumu: 11:7
nchito za atumiki othandiza: 6:12
oyang’anila: 5:29-34
Ubatizo
ana: masa. 179-181
kuikidwa kukhala mtumiki: 8:3
ofalitsa osabatizika: masa. 182-184
pa misonkhano yadela, yacigawo: 7:24, 26
tanthauzo la: 8:16-18
mafunso okambilana: masa. 185-207
Ukhondo; Ciyelo
ciyelo ca kuthupi: 13:8-12
ciyelo m’makhalidwe, kuuzimu: 13:6-7
Nyumba ya Ufumu: 11:7-8
Umutu
m’banja: 15:9-10
m’gulu la Yehova: 1:9-10; 2:5, 9-10; 15:1-2
olamulila akulu-akulu: 15:11
Utumiki wa nchito ya mamangidwe: 10:21-23
Kagulu ka Mamangidwe: 10:23
mtumiki wa nchito ya mamangidwe wocokela ku dziko lina: 10:23
mtumiki wa nchito ya mamangidwe: 10:23
Wothandizila mu Dipatimenti ya Mapulani na Mamangidwe: 10:23
wothandizila pa nchito ya mamangidwe:10:23
Utumiki wa pa Beteli: 10:19-20
Woyang’anila dela
kucezela mipingo: 5:41-48
kufunsila kuti muwonjezele utumiki: 10:6, 10, 16, 20
kum’celeza: 5:50
ndiye amavomeleza kupempha mpingo watsopano: 7:22
tumagulu:9:44
Woyang’anila Utumiki: 5:28, 32; 9:31, 37, 45
Yehova Mulungu
kumuyandikila: 17:1-3
Mfumu ya Cilengedwe Conse: 15:1-4
Yesu Khristu
kugonjela Yehova: 15:5
Mkulu wa Ansembe: 2:4
Muwomboli: 2:3
Zikwati: 11:10-11
Zilengezo
cidzudzulo: 14:24
kubwezeletsa: 14:36
kucotsa mu mpingo: 14:29
ofalitsa osabatizika: 8:12; 14:39-40
zopeleka: 12:6
kudzilekanitsa: 14:33
Zocitika za kusukulu: 13:22-24
Zolinga
kudziikila zolinga zimene tingakwanitse: 8:37
kufunika kwake: 10:24-26
kukatumikila kumalo osoŵa: 10:6-9
kuphunzila cinenelo cina: 10:10
masukulu a zaumulungu: 10:17-18
nchito ya m’dela: 10:16
ofalitsa: 10:4-5
umishonale: 10:15
upainiya: 10:11-14
Utumiki wa pa Beteli: 10:19-20
utumiki wa mamangidwe: 10:21-23
Zopeleka: 3:13; 11:6-7, 15; 12:2-11
Zosangulutsa na zosangalatsa: 13:15-21