LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w13 7/1 masa. 1-2
  • Zamkati

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zamkati
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
w13 7/1 masa. 1-2

Zamkati

July 1, 2013

Kodi Muyenela Kukhulupilila Cipembedzo?

© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. All rights reserved.

NKHANI ZOPHUNZILA

SEPTEMBER 2-8, 2013 | TSAMBA 9 • NYIMBO: 128, 101

“Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzacitika Liti?”

SEPTEMBER 9-15, 2013 | TSAMBA 15 • NYIMBO: 30, 109

“Dziŵani Kuti Ine Ndili Pamodzi Ndi Inu Masiku Onse”

Nkhani izi zidzafotokoza mbali zina za Mateyu caputala 24 ndi 25. Zikufotokoza kamvedwe katsopano ponena za nthawi pamene zocitika za mu ulosi wa Yesu wa masiku otsiliza, ndi za m’fanizo la tiligu ndi namsongole zidzacitika. Nkhani zimenezi zikuonetsanso mmene ifeyo tingapindulile ndi kamvedwe katsopano kameneka.

SEPTEMBER 16-22, 2013 | TSAMBA 21 • NYIMBO: 108, 117

Kudyetsa Anthu Ambili mwa Kugwilitsila Nchito Anthu Ocepa

SEPTEMBER 23-29, 2013 | TSAMBA 26 • NYIMBO: 107, 116

“Ndani Kweni-kweni Amene Ali Kapolo Wokhulupilika ndi Wanzelu?”

Pamene Yesu anapeleka cakudya kwa khamu la anthu mozizwitsa, ndiponso pamene anali kupeleka cakudya ca kuuzimu kwa otsatila ake, iye anali kutsatila njila ina yake. Njila imeneyo inali ya kudyetsa anthu ambili mwa kugwilitsila nchito anthu ocepa. Nkhani yoyamba idzafotokoza za anthu ocepa amene iye anagwilitsila nchito kupeleka cakudya ca kuuzimu kwa otsatila ake odzozedwa m’nthawi ya atumwi. Nkhani yaciŵili idzafotokoza funso lofunika kwambili ili: Kodi ndi anthu ocepa ati amene Kristu amagwilitsila nchito kutipatsa cakudya ca kuuzimu masiku ano?

NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO

Cifukwa Cake Muyenela Kucidziŵa Bwino Cipembedzo Canu 3

Kodi Cipembedzo Mungacikhulupilile Pankhani ya Ndalama? 4

Kodi Cipembedzo Mungacikhulupilile Pankhani ya Nkhondo? 5

Kodi Cipembedzo Mungacikhulupilile Pankhani ya Makhalidwe? 6

Kodi Pali Cipembedzo Cimene Mungakhulupilile? 7

M’bale Watsopano wa m’Bungwe Lolamulila 8

Kuyankha Mafunso a m’Baibo 32

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani