Zamkati
November 1, 2013
Mabodza Amene Amalepheletsa Anthu Kukonda Mulungu
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. All rights reserved.
NKHANI ZOPHUNZILA
DECEMBER 30, 2013–JANUARY 5, 2014 | TSAMBA 3 • NYIMBO: 67, 81
“Khalani Maso Kuti Musanyalanyaze Kupemphela”
Kukhala maso mwakuuzimu n’kofunika kwambili pamene mapeto a dongosolo loipa la Satana akuyandikila. Nkhani imeneyi ifotokoza mmene kupemphela nthawi zonse kungatithandizile kukhalabe maso mwa kuuzimu.
JANUARY 6-12, 2014 | TSAMBA 10 • NYIMBO: 119, 32
Mmene Tingayembekezele Mulungu Moleza Mtima
M’nkhani iyi, tidzakambilana mmene tingapindulile ndi citsanzo ca mneneli Mika ca kuleza mtima. Tidzaphunzilanso zocitika zimene zidzaonetsa kuti Yehova watsala pang’ono kuononga dongosolo loipali la zinthu. Tidzaonanso mmene tingaonetsele kuti timayamikila kuleza mtima kwa Mulungu.
JANUARY 13-19, 2014 | TSAMBA 16 • NYIMBO: 43, 123
Kodi Abusa 7 ndi Atsogoleli 8 Ndani Masiku Ano?
Timaphunzila zinthu zambili zothandiza tikamaŵelenga zimene zinacitika pamene Senakeribu anaukila Yerusalemu m’nthawi ya Hezekiya. Nkhani imeneyi ili ndi mfundo zothandiza kwambili kwa abale amene ali ndi udindo woweta nkhosa mumpingo.
JANUARY 20-26, 2014 | TSAMBA 21 • NYIMBO: 125, 122
JANUARY 27, 2014–FEBRUARY 2, 2014 | TSAMBA 26 • NYIMBO: 5, 84
Abusa, Tsanzilani Abusa Aakulu
Nkhani yoyamba m’nkhani ziŵili izi ifotokoza mmene Yehova ndi Yesu amawetela nkhosa zao padziko lapansi masiku ano ndipo ionetsanso mmene nkhosa zimaonetsela kuyamikila cisamalilo cao. Nkhani yotsatila idzafotokoza maganizo amene akulu mumpingo afunika kuyesetsa kukhala nao pamene akutumikila monga abusa aang’ono.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
Cifukwa Cake Ambili Amaona Kuti Kukonda Mulungu N’kovuta 3
Bodza Lakuti Mulungu Alibe Dzina 4
Bodza Lakuti Mulungu Ndi Wosamvetsetseka 4
Bodza Lakuti Mulungu Ndi Wankhanza 5