Ofalitsa agaŵila kabuku ka Uthenga Wabwino ku Azerbaijan
Maulaliki a Citsanzo
GALAMUKANI!
Funso: N’ciani cingatithandize kuseŵenzetsa nthawi mwanzelu?
Lemba: Mlal. 4:6
Cogaŵila: Galamukani! iyi ionetsa mmene tingagaŵile bwino nthawi.
PHUNZITSANI COONADI
Funso: N’cifukwa ciani tili na moyo?
Lemba: Sal. 37:29
Coonadi: Mulungu analenga anthu kuti akhale padziko lapansi kwamuyaya.
UTHENGA WABWINO WOCOKELA KWA MULUNGU
Funso: Muganiza n’kuti kumene tingapeze uthenga wabwino? [Mtambitseni vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kumvelako Uthenga Wabwino?]
Lemba: Yes. 52:7
Cogaŵila: Kabukuka kali na “uthenga wabwino wa zinthu zabwino” wocokela m’Baibo.
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: