January 27–February 2
GENESIS 9-11
Nyimbo 101 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Padziko Lonse Lapansi Panali Cilankhulo Cimodzi”: (10 min.)
Gen. 11:1-4—Anthu ena anaganiza zomanga mzinda na nsanja yake motsutsana na cifunilo ca Mulungu (it-1 239; it-2 202 ¶2)
Gen. 11:6-8—Yehova anasokoneza citundu cawo (it-2 202 ¶3)
Gen. 11:9—Anthuwo analeka kumanga nsanjayo na mzinda wake, ndipo anabalalikana (it-2 472)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 9:20-22, 24, 25—N’cifukwa ciani Nowa anatembelela Kanani m’malo mwa Hamu? (it-1 1023 ¶4)
Gen. 10:9, 10—Kodi Nimurodi anali “mlenje wamphamvu wotsutsana na Yehova” m’njila yotani? (it-2 503)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni cuma ca kuuzimu citi cimene mwapeza ponena za Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 10:6-32 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi, ndiyeno funsani omvetsela mafunso otsatilawa: N’ciani caonetsa kuti ofalitsawa anakonzekela pamodzi ulendo wobwelelako umenewu? Kodi m’baleyu wagaŵila motani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu na kuyambitsa phunzilo la Baibo?
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo a ulendo wobwelelako waciŵili, ndiyeno yambitsani phunzilo la Baibo mwa kuseŵenzetsa buku lakuti Zimene Baibulo Ingatiphunzitse. (th phunzilo 2)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Khalani Mmisili Waluso”: (15 min.) Nkhani yokambilana, yokambiwa na woyang’anila nchito.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 101
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 56 na Pemphelo