LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g20 na. 1 tsa. 16
  • “Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”
  • Galamuka!—2020
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • KWA OKWATILANA
  • KWA MAKOLO
  • KWA ACICEPELE
  • Kodi Mungakonde Kudziŵa Zambili?
    Galamuka!—2021
  • Ciŵelengelo ca Acinyamata Odwala Matenda a Maganizo Cikuculuka—Kodi Baibo Ikutipo Ciyani?
    Nkhani Zina
  • Kulemekezana m’Banja
    Galamuka!—2024
  • Pezani Nzelu Zothandiza pa Umoyo pa JW.ORG
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Galamuka!—2020
g20 na. 1 tsa. 16

MTIMA WODEKHA NDIWO MOYO WA MUNTHU”

Mwamuna na mkazi wake aŵelenga Baibo capamodzi pa tabuleti yawo.

Mawu amenewa opezeka pa Miyambo 14:30, analembedwa pafupi-fupi zaka 3,000 zapitazo! Ndipo amaonetsa kuti malangizo a m’Baibo ni othandiza nthawi zonse. Ngati mufuna kuphunzila zambili, yendani pa webusaiti ya jw.org ku Chichewa. Mudzapezapo mavidiyo, zithunzi na mavidiyo a tukadoli, kufunsa anthu mafunso, komanso nkhani zosiyana-siyana zothandiza, zimene ziphatikizapo nkhani zimene zingakuthandizeni kucepetsa nkhawa. Zina mwa nkhani zimene mudzapeza ni izi:

KWA OKWATILANA

  • Kuthetsa Mikangano

  • Zimene Mungachite Kuti Muzigwirizana ndi Achibale

  • Kodi Mungatani Kuti Musamasunge Chakukhosi?

KWA MAKOLO

  • Zimene Mungachite Kuti Muzimasukirana ndi Mwana Wanu

  • Ngati Mwana Wanu Wamkazi Akuvutika Maganizo

  • Phunzitsani Ana Anu Kuti Azigwiritsa Ntchito Intaneti Moyenera

KWA ACICEPELE

  • Kodi Mungatani Kuti Anzanu Asiye Kukuvutitsani?

  • Kodi Ndingatani Kuti Ndizigona Mokwanira?

  • N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kukhala Mwamtendere ndi Abale Anga?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani