Otonyi-eda khani khani da sanja ya olonda 2022
Tonyi-eda khani iliyetene eneyo ikumi-iwe
PUZIRO LA SANJA YA OLONDA
MOYO WACHIKIRISTU NA MAKALELO
Anapatsa Agalu Anga Mabisiketi (ulaliki wa vashelefu), Epulo
Kodi Muli Okozeya “Zawachela Ilambo Yavati?” Dizembala
“Lamulo la Kukoma Mtima Kosatha” Lizikutsogolerani, Juni
N’chifukwa Chiyani Masiku Ano Sitimenya Nkhondo Ngati Mmene Ankachitira Aisiraeli? Okotobala
Zimene Zingatithandize Tikakhala ndi Nkhawa, Epulo
KODI MUNOIZIWA?
Kodi Aroma ankalola kuti munthu amene waphedwa popachikidwa pamtengo, ngati mmene zinalili ndi Yesu, aikidwe m’manda ngati anthu ena onse? Juni
Kodi kale anthu ankadziwa bwanji pamene payambira mwezi kapena chaka? Juni
Kodi pi vyoona ira wookala muthu oromoliwa Moredekai? Novembala
N’chifukwa chiyani zinali zothandiza kuti munthu azitha kupereka njiwa kapena nkhunda monga nsembe? Febuluwale
N’chifukwa chiyani Aisiraeli ankapereka malowolo? Febuluwale
MBONI DA YEHOVA
1922 — Zaka 100 Zapitazo, Okotobala
LIMBILI LA MOYWANGA
Ndakhala Ndikusangalala Kuphunzira Komanso Kuphunzitsa Zokhudza Yehova (L. Weaver, Jr.), Septembala
Ndinalola Kuti Yehova Azinditsogolera pa Moyo Wanga (K. Eaton), Julayi
Ndinapeza Chinthu Chabwino Kwambiri Kuposa Kukhala Dokotala (R. Ruhlmann), Febuluwale
“Ndoofuna Tumikela Yehova” (D. Van Marl), Novembala
VYOFUKA VYOKUMELA WA OWELENGA
Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani ya malumbiro? Epulo
Kodi Yesu ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti: “Musaganize kuti ndinabweretsa mtendere”? (Mat 10:34, 35), Julayi
Kodi mtumwi Paulo ankatanthauza chiyani pomwe anadzitchula kuti anali ngati “khanda lobadwa masiku asanakwane”? (1 Akor. 15:8), Septembala
Kodi ndi anthu ati omwe adzaukitsidwire padzikoli, nanga kuuka kwake kudzakhala kotani? Septembala
Kodi wolemba masalimu Davide, ookokomeza kapena awonga vyongo vyevyo pivyo-owandeya vevo awonga liye ira unoza atamande Mulungu mpakana muyaya, n’nga mwemo vilembiwileathu va lemba la Salimo 61:8?, Dizembala
N’chifukwa chiyani lemba la 2 Samueli 21:7-9, limanena kuti Davide ‘anamvera chisoni Mefiboseti’ koma kenako anapereka Mefiboseti kuti aphedwe?, Marichi
Ngati Mkhristu wathetsa banja osati pa zifukwa za m’Malemba n’kukwatirana ndi munthu wina, Epulo
KHANI DOFUNJEDA
Achinyamata, Pitirizani Kupita Patsogolo Mwauzimu Pambuyo Pobatizidwa, Ogaste
Akulu, Pitirizani Kutsanzira Mtumwi Paulo, Marichi
Anthu a Yehova Amakonda Chilungamo, Ogaste
Chifukwa Chake Timapezeka pa Chikumbutso, Januwale
‘Imva Mawu a Anthu Anzeru,’ Febuluwale
Kamulole Ira Iliyetene Iwumwalani-eni na Yehova, Novembala
Kodi Chikondi Chingatithandize Bwanji Kuti Tisamachite Mantha?, Juni
Kodi Dzina Lanu Lili “M’buku la Moyo”? Septembala
Kodi Malangizo Amene Mumapereka ‘Amasangalatsa Mtima’? Febuluwale
Kodi Mukuona Zimene Zekariya Anaona? Marichi
Kodi Mumakhulupirira Kuti Yehova Amachita Zinthu M’njira Yoyenera? Febuluwale
Kodi Ndinu “Chitsanzo . . . M’kalankhulidwe”? Epulo
Kulambira Koona Kumachititsa Kuti Muzisangalala Kwambiri, Marichi
‘Kuthandiza Anthu Ambiri Kuti Akhale Olungama,’ Septembala
Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikonda Yehova, Mey
Mukalengave oganiza pama mwashishiwanga, Novembala
Mukami-edenga Amo-i Vilela Vathawi Dorucha, Dizembala
Mukhoza ‘Kuvula Umunthu Wakale,’ Marichi
Mungapeze Chimwemwe Chenicheni, Okotobala
Munokoza Fwanya Murendele Vathawi ya Mavuto, Dizembala
“Muzigwiritsa Ntchito Bwino Nthawi Yanu,” Januwale
Muzikhulupirira Abale Anu, Septembala
Muzisangalala ndi Zonse Zomwe Mukuchita Potumikira Yehova, Epulo
Muzisonyeza Kuti Ndinu Wodalirika, Septembala
Muzitsanzira Yesu Potumikira Ena, Febuluwale
Muziyamikira Mwayi Wanu wa Pemphero, Julayi
Mwemo Yehova Munanikami-edela Liye Kwakwaneli-eda Utumiki-u, Novembala
Ninokoza Kaana Moyo Mpakana Walewale, Dizembala
Nzeru Yeniyeni Ikufuula, Okotobala
Nzeru Zothandiza pa Moyo Wathu, Mey
Odala Ndi Anthu Okhulupirika Kwa Yehova, Okotobala
“Ofunafuna Yehova Sadzasowa Chilichonse Chabwino,” Januwale
Pitirizani Kuvala “Umunthu Watsopano” Pambuyo Pobatizidwa, Marichi
‘Pitirizani Kuyendabe M’choonadi,’ Ogaste
Pitirizani “Kulimbikitsana,” Ogaste
Pitirizani Kulimbitsa Chiyembekezo Canu, Okotobala
Tingatani Kuti Tizikhala ndi Zolinga Zauzimu N’kumazikwaniritsa?, Epulo
Tizithandiza Mtsogoleri Wathu Yesu, Julayi
Ufumu Ukulamulira! Julayi
Ulosi Wakalekale Umene Umakukhudzani, Julayi
Yehova Amadalitsa Anthu Omwe Amakhululuka, Juni
Yehova Amakhululuka Kwambiri Kuposa Aliyense, Juni
Yehova Amayang’anira Anthu Ake, Ogaste
“Yembekezera Yehova,” Juni
Zimene Tingachite Kuti Tizisangalalabe Tikakumana ndi Mayesero, Novembala
Zimene Tingaphunzire Kuchokera kwa Mng’ono Wake wa Yesu, Januwale
Zimene Tikuphunzira pa Misozi ya Yesu, Januwale
Zimene Azimayi Angaphunzire kwa Yunike, Epulo
Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakhudzanso Adani a Mulungu, Mey
Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakhudza Tsogolo Lanu, Mey
Zimene Zili M’buku la Chivumbulutso Zimakukhudzani, Mey
“Weyo Unoza Ukale Na Miyo M’Paradaizo,” Dizembala