Genesis 24:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiponso Sara mkazi wake anamuberekera mbuyangayo mwana wamwamuna, mbuyangayo atakalamba.+ Mbuyangayo adzapatsa mwanayo zonse zimene ali nazo.+ Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+ Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
36 Ndiponso Sara mkazi wake anamuberekera mbuyangayo mwana wamwamuna, mbuyangayo atakalamba.+ Mbuyangayo adzapatsa mwanayo zonse zimene ali nazo.+
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.