Genesis 35:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni. Genesis 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Isakara+ anali Tola,+ Puva,+ Yabi ndi Simironi.+ Genesis 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Isakara+ ndi bulu wa mafupa olimba, amagona pansi atasenza matumba a katundu uku ndi uku. Deuteronomo 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kwa Zebuloni anati:+“Kondwera Zebuloni iwe, pa maulendo ako,+Ndiponso iwe Isakara, m’mahema ako.+ 1 Mbiri 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse. Chivumbulutso 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mu fuko la Simiyoni,+ 12,000.Mu fuko la Levi,+ 12,000.Mu fuko la Isakara,+ 12,000.
23 Ana aamuna amene Leya anaberekera Yakobo anali Rubeni+ mwana wake woyamba, Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara ndi Zebuloni.
32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse.