Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma kutacha m’mawa, Yakobo anadabwa kuona kuti ali ndi Leya! Ataona zimenezi anakafunsa Labani kuti: “Ndiye chiyani mwachitachi? Kodi si Rakele amene ndakugwirirani ntchito? N’chifukwa chiyani mwandipusitsa chonchi?”+

  • Genesis 31:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Nyama yanu iliyonse imene inakhadzulidwa ndi chilombo sindinaibweretse kwa inu.+ Ndinali kuitenga kukhala yanga. Kaya ina ibedwe usana kapena usiku, munali kundiuza kuti ndikulipireni.+

  • Deuteronomo 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Uzim’patsa malipiro ake+ tsiku lililonse, ndipo dzuwa lisalowe usanam’patse malipiro ake chifukwa iye ndi wovutika. Iye akuyembekezera malipiro akewo mwachidwi, ndipo angafuule kwa Yehova chifukwa cha zimene iweyo wam’chitira,+ iwe n’kupezeka kuti wachimwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena