Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma bambo anu akhala akundipusitsa, ndipo asintha malipiro anga maulendo 10. Ngakhale ndi choncho, Mulungu sanawalole kuti andichite choipa.+

  • Genesis 31:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Mulungu wa bambo anga,+ Mulungu wa Abulahamu, Mulungu amene Isaki anali kumuopa,+ akanapanda kukhala kumbali yanga, bwenzi mutandibweza kwathu chimanjamanja. Koma Mulungu waona kusautsika kwanga ndi ntchito zimene ndagwira molimbika, n’chifukwa chake anakudzudzulani usiku wapitawu.”+

  • Levitiko 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “‘Musabe,+ musanamizane+ ndipo aliyense asachitire mnzake chinyengo.+

  • Mateyu 5:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Tangotsimikizani kuti mukati Inde akhaledi Inde, ndipo mukati Ayi akhaledi Ayi,+ pakuti mawu owonjezera pamenepa achokera kwa woipayo.+

  • 2 Akorinto 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri,+ ndipo sitikuyenda mwachinyengo komanso sitikupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pamaso pa Mulungu, takhala chitsanzo chabwino kwa chikumbumtima cha munthu aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena