Ekisodo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukamuzunza ngakhale pang’ono, iye n’kundilirira, ndidzamva ndithu kulira kwake.+ Yobu 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kuti achititse kulira kwa wonyozeka kupita kwa iye.Choncho iye amamva kulira kwa osautsika.+ Salimo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndapereka moyo wanga kwa inu Yehova.+ Salimo 86:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Sangalatsani mtima wa ine mtumiki wanu,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu Yehova.+ Miyambo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+ ndipo adzalanda moyo wa amene akuwabera.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.
4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.