Genesis 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yakobo anamupsera mtima kwambiri Rakele n’kumuyankha kuti:+ “Kodi ine ndine Mulungu amene akukulepheretsa kuberekayo?”+ Miyambo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kuzindikira kumachititsa munthu kubweza mkwiyo wake,+ ndipo kunyalanyaza cholakwa kumam’chititsa kukhala wokongola.+ Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwiyani, koma musachimwe.+ Dzuwa lisalowe muli chikwiyire,+
2 Pamenepo Yakobo anamupsera mtima kwambiri Rakele n’kumuyankha kuti:+ “Kodi ine ndine Mulungu amene akukulepheretsa kuberekayo?”+
11 Kuzindikira kumachititsa munthu kubweza mkwiyo wake,+ ndipo kunyalanyaza cholakwa kumam’chititsa kukhala wokongola.+