Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+ Salimo 95:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nyanja imene anapanga ndi yake,+Iye amenenso anapanga mtunda ndi manja ake.+
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+