Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano Mulungu anatcha mtundawo Dziko,+ koma madzi osonkhanawo anawatcha Nyanja.+ Ndipo Mulungu anaona kuti zili bwino.+

  • Yobu 38:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+

      Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+

  • Miyambo 8:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+

  • Yeremiya 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 ‘Kodi simundiopa?’+ watero Yehova. ‘Kapena kodi simukumva ululu waukulu chifukwa cha ine?+ Ine ndinaika mchenga kukhala malire a nyanja, malire okhalapo mpaka kalekale amene nyanjayo singadutse. Ngakhale kuti mafunde amawinduka sangadutse malirewo ndipo ngakhale amachita phokoso sangawapitirire.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena