Yesaya 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+ Mateyu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina,+ ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomezi+ m’malo osiyanasiyana. Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+ Machitidwe 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera mwa mzimu kuti padziko lonse lapansi kumene kuli anthu,+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi m’nthawi ya Kalaudiyo.
4 Dzikolo likulira+ ndipo likuzimiririka. Nthaka ya dziko lapansi yafota ndipo yazimiririka. Anthu apamwamba a m’dzikolo afota.+
7 “Mtundu udzaukirana ndi mtundu wina,+ ndipo ufumu udzaukirana ndi ufumu wina.+ Kudzakhala njala+ ndi zivomezi+ m’malo osiyanasiyana.
11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+
28 Mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera mwa mzimu kuti padziko lonse lapansi kumene kuli anthu,+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi m’nthawi ya Kalaudiyo.