Genesis 41:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Tsopano zaka 7 za njala zinayamba, monga Yosefe ananenera.+ Njalayo inafalikira m’mayiko onse, koma dziko lonse la Iguputo linali ndi chakudya.+ Genesis 42:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ana a Isiraeliyo anafika ku Iguputo limodzi ndi anthu ena okagula tirigu, chifukwa m’dziko la Kanani munali njala.+
54 Tsopano zaka 7 za njala zinayamba, monga Yosefe ananenera.+ Njalayo inafalikira m’mayiko onse, koma dziko lonse la Iguputo linali ndi chakudya.+
5 Ndiyeno ana a Isiraeliyo anafika ku Iguputo limodzi ndi anthu ena okagula tirigu, chifukwa m’dziko la Kanani munali njala.+