Genesis 41:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, ndithudi padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka chija m’dziko la Iguputo sichidzakumbukika m’pang’ono pomwe, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+ Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+
30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, ndithudi padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka chija m’dziko la Iguputo sichidzakumbukika m’pang’ono pomwe, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+
11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+