Genesis 41:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Komanso, anthu a padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, pakuti njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+ Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+
57 Komanso, anthu a padziko lonse lapansi anayamba kubwera ku Iguputo kudzagula chakudya kwa Yosefe, pakuti njalayo inali itafika poipa kwambiri padziko lonse lapansi.+
11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+