2 Atesalonika 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pomalizira abale, pitirizani kutipempherera+ kuti mawu a Yehova*+ apitirize kufalikira mofulumira+ ndi kulemekezedwa ngati mmene akuchitira pakati panu.
3 Pomalizira abale, pitirizani kutipempherera+ kuti mawu a Yehova*+ apitirize kufalikira mofulumira+ ndi kulemekezedwa ngati mmene akuchitira pakati panu.