35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsalira ku Antiokeya.+ Ndipo iwo pamodzi ndi enanso ambiri anali kuphunzitsa ndi kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.+
8 Ndipotu, si kuti mawu a Yehova+ ochokera kwa inu amveka ku Makedoniya ndi ku Akaya kokha ayi, koma kwina kulikonse chikhulupiriro+ chanu mwa Mulungu chafalikira,+ moti ife sitikufunika kunenapo kanthu.