Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pobwerera, zinachitika n’zakuti, titafika pamalo ogona+ n’kumasula matumba athu, tinangoona kuti ndalama za aliyense zili pakamwa pa thumba lake, zonse malinga ndi kulemera kwake. Choncho tabwera nazo kuti tizibweze tokha.+

  • Miyambo 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wolungama amasamalira moyo wa chiweto chake,+ koma chisamaliro cha anthu oipa n’chankhanza.+

  • Yeremiya 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikanakonda kukhala ndi malo a m’chipululu ogona anthu apaulendo.+ Pamenepo ndikanasiya anthu anga ndi kuwachokera, pakuti onsewo ndi achigololo,+ gulu la anthu ochita zachinyengo.+

  • Yeremiya 41:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo anakakhala kumalo ogona a Chimamu pafupi ndi Betelehemu+ ndi cholinga choti apitirize ulendo wawo kukalowa mu Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena