Genesis 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+ Miyambo 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wokana kugulitsa mbewu zake kwa anthu, anthuwo adzam’temberera. Koma wolola kuzigulitsa adzalandira madalitso.+ Machitidwe 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+
5 Koma musadzimvere chisoni+ kapena kudzipsera mtima kuti munandigulitsa kuno. Mulungu ndiye ananditumiza patsogolo panu kuti ndidzapulumutse miyoyo yanu.+
26 Wokana kugulitsa mbewu zake kwa anthu, anthuwo adzam’temberera. Koma wolola kuzigulitsa adzalandira madalitso.+
11 Tsopano munagwa njala yaikulu mu Iguputo ndi mu Kanani monse, inde chisautso chachikulu. Ndipo makolo athuwo sanali kupeza chakudya.+