Levitiko 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Malamulo angawa muziwasunga: Musakweranitse ziweto zanu zosiyana. Pobzala mbewu m’munda mwanu musasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+ Salimo 104:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+
19 “‘Malamulo angawa muziwasunga: Musakweranitse ziweto zanu zosiyana. Pobzala mbewu m’munda mwanu musasakanize mitundu iwiri yosiyana.+ Ndipo musamavale chovala cha ulusi wa mitundu iwiri yosakaniza.*+
14 Amameretsa msipu kuti nyama zidye,+Ndipo amameretsa mbewu kuti anthu agwiritse ntchito.+Amachita zimenezi kuti chakudya chituluke m’nthaka,+