Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 46:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+

  • Genesis 47:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano nthawi inayandikira yakuti Isiraeli amwalire.+ Ndiye anaitana mwana wake Yosefe n’kumuuza kuti: “Ngati ungandikomere mtima, ika dzanja lako pansi pa ntchafu yanga.+ Ulumbire kuti udzandisonyeza kukoma mtima kosatha ndipo udzakhala wokhulupirika kwa ine.+ Chonde, usadzandiike m’manda ku Iguputo kuno.+

  • Yohane 19:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano zitatha izi, Yosefe wa ku Arimateya, amene anali wophunzira wa Yesu koma wamseri chifukwa anali kuopa Ayuda,+ anapempha Pilato kuti amulole kuti akachotse mtembo wa Yesu, ndipo Pilato anamupatsa chilolezo.+ Choncho anafika ndi kuchotsa mtembowo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena