Salimo 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munamupatsa mphamvu kuti alamulire ntchito za manja anu.+Mwaika zonse pansi pa mapazi ake:+ Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+ Yakobo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti anthu akhala akuweta mtundu uliwonse wa nyama zakutchire, mbalame, ndi zokwawa ndiponso zamoyo zam’nyanja.+
9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+
7 Pakuti anthu akhala akuweta mtundu uliwonse wa nyama zakutchire, mbalame, ndi zokwawa ndiponso zamoyo zam’nyanja.+