Genesis 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+ Ekisodo 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu ake,+ moti Aiguputo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha,+ ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+ Salimo 105:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.
14 Koma mtundu umene adzautumikirewo ndidzauweruza.+ Pambuyo pake, iwo adzachokako ndi katundu wochuluka.+
36 Choncho Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima anthu ake,+ moti Aiguputo anawapatsa zinthu zonse zimene anapempha,+ ndipo iwo anatenga zinthu zambiri za Aiguputo.+
37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.