Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Nadabu ndi Abihu,+ ana a Aroni, aliyense anatenga chofukizira,+ n’kuikamo moto ndi zofukiza+ pamwamba pake. Pamenepo anayamba kupereka zofukiza pamoto wosaloledwa+ ndi Yehova, umene iye sanawalamule.

  • 2 Mbiri 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kenako iwo anatsutsa mfumu Uziya+ n’kuiuza kuti: “Mfumu Uziya, si ntchito yanu+ kufukiza kwa Yehova koma ntchito yofukizayi ndi ya ansembe, ana a Aroni,+ amene anayeretsedwa. Tulukani m’nyumba yopatulikayi popeza mwachita zosakhulupirika, ndipo sizikubweretserani ulemerero uliwonse+ pamaso pa Yehova Mulungu.”

  • Ezekieli 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndinaonanso akuluakulu 70+ a nyumba ya Isiraeli ataimirira. Yaazaniya mwana wa Safani+ anali ataima pakati pawo. Iwo anaima pamaso pa zojambulazo, aliyense atanyamula chiwaya chofukizira nsembe m’manja mwake. Utsi wonunkhira wa zofukizazo unali kukwera m’mwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena