Ekisodo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atsikanawo atafika kunyumba kwa bambo wawo Reueli,+ iye anadabwa ndipo anati: “Bwanji mwabwerako mwamsanga chonchi lero?” Ekisodo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi Aisiraeli, anthu a Mulungu, ndi mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+ Numeri 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Mose anauza Hobabu yemwe anali mwana wa Reueli+ Mmidiyani, mpongozi wake kuti: “Tikusamukira kumalo amene Yehova anati, ‘Ndidzawapereka kwa inu.’+ Tiyeni tipite limodzi, ndipo tidzakuchitirani zabwino ndithu,+ pakuti Yehova analonjeza Aisiraeli zabwino.”+
18 Ndiyeno atsikanawo atafika kunyumba kwa bambo wawo Reueli,+ iye anadabwa ndipo anati: “Bwanji mwabwerako mwamsanga chonchi lero?”
18 Tsopano Yetero, wansembe wa ku Midiyani, apongozi ake a Mose,+ anamva zonse zimene Mulungu anachitira Mose ndi Aisiraeli, anthu a Mulungu, ndi mmene Yehova anawatulutsira ku Iguputo.+
29 Ndiyeno Mose anauza Hobabu yemwe anali mwana wa Reueli+ Mmidiyani, mpongozi wake kuti: “Tikusamukira kumalo amene Yehova anati, ‘Ndidzawapereka kwa inu.’+ Tiyeni tipite limodzi, ndipo tidzakuchitirani zabwino ndithu,+ pakuti Yehova analonjeza Aisiraeli zabwino.”+