Ekisodo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ukalankhule naye ndi kumuuza zokanena.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye pamene mukulankhula,*+ ndipo ndidzakuuzani zochita.+ Ekisodo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Aroni anawauza mawu onse amene Yehova anauza Mose,+ ndipo iye anachita zizindikiro+ pamaso pa anthuwo.
15 Ukalankhule naye ndi kumuuza zokanena.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye pamene mukulankhula,*+ ndipo ndidzakuuzani zochita.+
30 Pamenepo Aroni anawauza mawu onse amene Yehova anauza Mose,+ ndipo iye anachita zizindikiro+ pamaso pa anthuwo.