Ekisodo 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anam’tuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anam’lamula kuchita.+ Ekisodo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+
28 Atakumana, Mose anauza Aroni mawu onse a Yehova, yemwe anam’tuma.+ Anamuuzanso zizindikiro zonse zimene anam’lamula kuchita.+
7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+