Ekisodo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ukalankhule naye ndi kumuuza zokanena.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye pamene mukulankhula,*+ ndipo ndidzakuuzani zochita.+ Ekisodo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+
15 Ukalankhule naye ndi kumuuza zokanena.+ Ineyo ndidzakhala ndi iwe pamodzi ndi iye pamene mukulankhula,*+ ndipo ndidzakuuzani zochita.+
7 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Taona, ndakuika kuti ukhale Mulungu kwa Farao,+ ndipo Aroni m’bale wako akhala mneneri wako.+