1 Mafumu 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni, Salimo 106:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo anali kuchititsa kuti anthu onse owagwira ukapoloAwamvere chisoni.+ 1 Petulo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ omverana chisoni, okonda abale, achifundo chachikulu,+ ndiponso amaganizo odzichepetsa.+
50 Mukhululukire+ anthu anu amene anakuchimwirani.+ Muwakhululukirenso chifukwa cha malamulo anu onse amene anaphwanya,+ komanso owagwirawo akamawaona azikhudzidwa mtima+ ndi kuwachitira chisoni,
8 Pomaliza, nonsenu mukhale amaganizo amodzi,+ omverana chisoni, okonda abale, achifundo chachikulu,+ ndiponso amaganizo odzichepetsa.+