Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pita, ukasonkhanitse akulu a Isiraeli ndi kuwauza kuti, ‘Yehova Mulungu wa makolo anu, Mulungu wa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, anaonekera kwa ine+ n’kundiuza kuti: “Ndithu, ndidzakulanditsani ndi kuchitapo kanthu+ pa zonse zimene akukuchitirani mu Iguputo.

  • Ekisodo 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho Mose anatsika n’kuitanitsa akulu onse+ a anthu, ndipo anawauza mawu onse amene Yehova anam’lamula.+

  • Numeri 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena