Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 50:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Potsirizira pake, Yosefe anauza abale ake kuti: “Ine ndikufa, koma Mulungu adzakucheukirani,+ ndipo adzakutulutsani ndithu m’dziko lino. Adzakupititsani kudziko limene analonjeza polumbira kwa Abulahamu, kwa Isaki ndi kwa Yakobo.”+

  • Ekisodo 13:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho Mose anatenga mafupa a Yosefe chifukwa Yosefe analumbiritsa ana a Isiraeli, kuti: “Ndithudi, Mulungu adzakukumbukirani,+ ndipo pochoka kuno mudzatenge mafupa anga.”+

  • Salimo 80:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu wa makamu, chonde bwererani.+

      Yang’anani pansi pano muli kumwambako, ndipo onani ndi kusamalira mtengo wa mpesa uwu.+

  • Luka 1:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena