Genesis 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+ Genesis 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo anadalitsa Yosefe,+ kuti: “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala m’busa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+
17 Pamene Abulamu anali ndi zaka 99, Yehova anaonekera kwa iye n’kumuuza kuti:+ “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Yenda pamaso panga ndipo ukhale wolungama.+
15 Pamenepo anadalitsa Yosefe,+ kuti: “Mulungu woona amene makolo anga Abulahamu ndi Isaki anayenda pamaso pake,+Mulungu woona amene wakhala m’busa wanga moyo wanga wonse mpaka lero,+