Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko. Salimo 105:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anachita zimenezi kuti asunge malangizo ake,+Ndi kusunga malamulo ake.+Tamandani Ya, anthu inu!+
10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.