Ekisodo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+ Ekisodo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mose analankhula mawu amenewa kwa ana a Isiraeli, koma iwo sanamvere Mose chifukwa chokhumudwa ndiponso chifukwa cha ntchito yowawa ya ukapolo.+ Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+ Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+
21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+
9 Kenako Mose analankhula mawu amenewa kwa ana a Isiraeli, koma iwo sanamvere Mose chifukwa chokhumudwa ndiponso chifukwa cha ntchito yowawa ya ukapolo.+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma n’kupsetsa mtima Mulungu?+ Kodi si anthu onse amene anatuluka m’dziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+