Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Mitundu yatheratu padziko lapansi.+ Salimo 146:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+
3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+