Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 81:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+

      Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+

      Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]

  • Salimo 102:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Musandibisire nkhope yanu pa tsiku limene ndili m’masautso aakulu.+

      Tcherani khutu lanu kwa ine.+

      Fulumirani kundiyankha pa tsiku limene ndikuitana.+

  • Danieli 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano ine ndikuika lamulo+ lakuti, anthu onse a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana amene anganene chilichonse chotsutsana ndi Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego ayenera kudulidwa nthulinthuli,+ ndipo nyumba zawo zisandutsidwe zimbudzi za anthu onse,+ pakuti palibe mulungu wina amene amatha kupulumutsa chotere.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena