Ekisodo 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Usabe.+ Aroma 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa malamulo onena kuti, “Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,+ Usabe,+ Usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili m’mawu awa akuti, “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+ 1 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akuba, aumbombo,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.+ Aefeso 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+ 1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+
9 Chifukwa malamulo onena kuti, “Usachite chigololo,+ Usaphe munthu,+ Usabe,+ Usasirire mwansanje,”+ ndiponso lamulo lina lililonse limene lilipo, chidule chake chili m’mawu awa akuti, “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+
28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+
15 Koma pasakhale wina wa inu wovutika+ chifukwa cha kupha munthu, kuba, kuchita choipa china kapena kulowerera nkhani za ena.+