Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno ndinauza Alevi+ kuti pobwera azidziyeretsa nthawi zonse+ komanso azilondera zipata za mzinda+ kuti tsiku la sabata likhale loyera.+ Inu Mulungu wanga, mundikumbukirenso+ pa zimenezi ndipo mundimvere chifundo malinga ndi kuchuluka kwa kukoma mtima kwanu kosatha.+

  • Yesaya 56:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Wodala ndi munthu amene amachita zimenezi,+ ndiponso mwana wa munthu amene amatsatira zimenezi,+ amene amasunga sabata kuti asalidetse,+ ndiponso amaletsa dzanja lake kuti lisachite choipa chilichonse.+

  • Yesaya 58:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Mukabweza phazi lanu chifukwa cha sabata, kuti musiye kuchita zokonda zanu pa tsiku langa lopatulika,+ sabatalo mukalitcha tsiku losangalatsa kwambiri, tsiku lopatulika ndi lolemekezeka la Yehova,+ ndipo mukalilemekeza m’malo moyenda njira zanu, m’malo mopeza zinthu zosangalatsa inuyo, ndiponso m’malo molankhula zopanda pake,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena